Genesis 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+ Numeri 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Chifukwa Yehova analephera kufikitsa anthuwo kudziko limene anawalumbirira, anangowaphera m’chipululu.’+
3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+
16 ‘Chifukwa Yehova analephera kufikitsa anthuwo kudziko limene anawalumbirira, anangowaphera m’chipululu.’+