Genesis 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanditcha wodala.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Aseri.*+ Yoswa 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Maere achisanu+ anagwera fuko la ana a Aseri,+ potsata mabanja awo.
13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanditcha wodala.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Aseri.*+