Ezekieli 45:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuchokera pa miyezo ya malo amenewa, udzayeze malo okwana mikono 25,000 m’litali ndi mikono 10,000 m’lifupi. M’malo amenewa mudzakhale malo opatulika amene ndi malo oyera koposa.+
3 Kuchokera pa miyezo ya malo amenewa, udzayeze malo okwana mikono 25,000 m’litali ndi mikono 10,000 m’lifupi. M’malo amenewa mudzakhale malo opatulika amene ndi malo oyera koposa.+