Genesis 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+ Yoswa 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mizinda ya fuko la ana a Benjamini potsata mabanja awo inali Yeriko,+ Beti-hogila, Emeki-kezizi,
18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+