Genesis 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+ Yoswa 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi
13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+
10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi