Ezekieli 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndithu Ine ndidzathetsa mwambi umenewu ndipo sadzaunenanso ngati mwambi mu Isiraeli.”’+ Koma uwauze kuti, ‘Masiku ayandikira+ ndipo zonse zotchulidwa m’masomphenya zichitikadi.’ Zefaniya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+
23 Chotero uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndithu Ine ndidzathetsa mwambi umenewu ndipo sadzaunenanso ngati mwambi mu Isiraeli.”’+ Koma uwauze kuti, ‘Masiku ayandikira+ ndipo zonse zotchulidwa m’masomphenya zichitikadi.’
14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+