Yeremiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Yeremiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bisalani, inu ana a Benjamini, thawani pakati pa Yerusalemu. Ku Tekowa+ imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+ Ku Beti-hakeremu+ kwezani moto wa chizindikiro, chifukwa chiwonongeko chachikulu, tsoka, lasuzumira kuchokera kumpoto.+
5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
6 Bisalani, inu ana a Benjamini, thawani pakati pa Yerusalemu. Ku Tekowa+ imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+ Ku Beti-hakeremu+ kwezani moto wa chizindikiro, chifukwa chiwonongeko chachikulu, tsoka, lasuzumira kuchokera kumpoto.+