Deuteronomo 28:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Udzafufuzafufuza masana ngati mmene wakhungu amafufuzirafufuzira mu mdima,+ ndipo sudzapambana. Iwe wekha udzakhala wodyeredwa ndi kulandidwa zinthu nthawi zonse, popanda wokupulumutsa.+ 2 Mbiri 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+ Maliro 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.
29 Udzafufuzafufuza masana ngati mmene wakhungu amafufuzirafufuzira mu mdima,+ ndipo sudzapambana. Iwe wekha udzakhala wodyeredwa ndi kulandidwa zinthu nthawi zonse, popanda wokupulumutsa.+
19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+
10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.