Ezekieli 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano akuluakulu a Isiraeli anabwera kwa ine n’kudzakhala pamaso panga.+ Ezekieli 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’chaka cha 7, m’mwezi wachisanu, pa tsiku la 10 la mweziwo, akuluakulu a Isiraeli anabwera kwa ine kudzafunsira kwa Yehova,+ ndipo anakhala pamaso panga.+
20 M’chaka cha 7, m’mwezi wachisanu, pa tsiku la 10 la mweziwo, akuluakulu a Isiraeli anabwera kwa ine kudzafunsira kwa Yehova,+ ndipo anakhala pamaso panga.+