Ezekieli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndili mkati moyang’ana, ndinangoona dzanja litatambasukira kwa ine.+ M’dzanjalo munali mpukutu wolembedwa.+ Danieli 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene anali kuchita zimenezi, zala za munthu zinaonekera ndipo zinayamba kulemba pafupi ndi choikapo nyale, papulasitala wa pakhoma* la nyumba ya mfumu,+ ndipo mfumuyo inaona dzanja limene linali kulembalo.
9 Ndili mkati moyang’ana, ndinangoona dzanja litatambasukira kwa ine.+ M’dzanjalo munali mpukutu wolembedwa.+
5 Pamene anali kuchita zimenezi, zala za munthu zinaonekera ndipo zinayamba kulemba pafupi ndi choikapo nyale, papulasitala wa pakhoma* la nyumba ya mfumu,+ ndipo mfumuyo inaona dzanja limene linali kulembalo.