Maliro 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wakunga uta wake ngati mdani.+ Dzanja lake lamanja+ lakonzeka ngati la mdani,+Ndipo wapitiriza kupha+ anthu onse ofunika kwambiri.Ukali wake waukhuthula ngati moto+ m’hema+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni. Maliro 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+
4 Wakunga uta wake ngati mdani.+ Dzanja lake lamanja+ lakonzeka ngati la mdani,+Ndipo wapitiriza kupha+ anthu onse ofunika kwambiri.Ukali wake waukhuthula ngati moto+ m’hema+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.
11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+