Ezekieli 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chamoyo chilichonse chinkapita kutsogolo basi.+ Zamoyozo zinali kupita kulikonse kumene mzimu wafuna kuti zipite.+ Zikamayenda sizinali kutembenuka.+ Ezekieli 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawilowo anali kulowera kumbali zawo zonse zinayi. Akamayenda, sanali kukhota chifukwa chakuti anali kulowera kumene mitu ya akerubiwo* yayang’ana. Akamayenda sanali kukhota.+
12 Chamoyo chilichonse chinkapita kutsogolo basi.+ Zamoyozo zinali kupita kulikonse kumene mzimu wafuna kuti zipite.+ Zikamayenda sizinali kutembenuka.+
11 Mawilowo anali kulowera kumbali zawo zonse zinayi. Akamayenda, sanali kukhota chifukwa chakuti anali kulowera kumene mitu ya akerubiwo* yayang’ana. Akamayenda sanali kukhota.+