Ezekieli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu inu okhala m’dziko la Isiraeli mukunena+ wakuti, ‘Masiku akupita+ koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani? 2 Petulo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene azidzati:+ “Kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, kuchokera tsiku limene makolo athu anamwalira, zinthu zonse zikupitirirabe chimodzimodzi ngati mmene zakhalira kuyambira pa chiyambi cha chilengedwe.”+
22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu inu okhala m’dziko la Isiraeli mukunena+ wakuti, ‘Masiku akupita+ koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani?
4 amene azidzati:+ “Kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, kuchokera tsiku limene makolo athu anamwalira, zinthu zonse zikupitirirabe chimodzimodzi ngati mmene zakhalira kuyambira pa chiyambi cha chilengedwe.”+