1 Mafumu 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Yehova anene kwa ine n’zimene ndikalankhule.”+ Yeremiya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana.’ Koma upite kwa anthu onse amene ndidzakutumako. Ndipo ukanene zonse zimene ndidzakulamula kuti ukanene.+
14 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Yehova anene kwa ine n’zimene ndikalankhule.”+
7 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana.’ Koma upite kwa anthu onse amene ndidzakutumako. Ndipo ukanene zonse zimene ndidzakulamula kuti ukanene.+