Hoseya 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi ina, mlonda+ wa Efuraimu anali ndi Mulungu wanga.+ Koma tsopano panjira zonse za mneneri,+ pali msampha wa wosaka mbalame.+ M’nyumba ya Mulungu wake muli chidani chachikulu.
8 Pa nthawi ina, mlonda+ wa Efuraimu anali ndi Mulungu wanga.+ Koma tsopano panjira zonse za mneneri,+ pali msampha wa wosaka mbalame.+ M’nyumba ya Mulungu wake muli chidani chachikulu.