Yesaya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Ambuye woona,+ Yehova wa makamu, akuchotsa mu Yerusalemu+ ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo. Akuchotsa mkate, madzi,+ Yeremiya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno akakufunsa kuti, ‘Tichoke kupita kuti?’ ukayankhe kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Woyenera kufa ndi mliri afe ndi mliri! Woyenera kufa ndi lupanga afe ndi lupanga! Woyenera kufa ndi njala yaikulu afe ndi njala yaikulu!+ Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo atengedwe kupita ku ukapolo!”’+
3 Tamverani! Ambuye woona,+ Yehova wa makamu, akuchotsa mu Yerusalemu+ ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo. Akuchotsa mkate, madzi,+
2 Ndiyeno akakufunsa kuti, ‘Tichoke kupita kuti?’ ukayankhe kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Woyenera kufa ndi mliri afe ndi mliri! Woyenera kufa ndi lupanga afe ndi lupanga! Woyenera kufa ndi njala yaikulu afe ndi njala yaikulu!+ Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo atengedwe kupita ku ukapolo!”’+