Ezekieli 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Amuna atatu awa: Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu,+ akanakhala m’dzikolo, iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+
14 “‘Amuna atatu awa: Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu,+ akanakhala m’dzikolo, iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+