Ekisodo 39:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anawomba mikanjo ya Aroni ndi ana ake ya ulusi wabwino kwambiri.+