Yeremiya 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chigololo chako,+ kumemesa* kwako,+ khalidwe lako lotayirira la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona zinthu zako zonyansa pamapiri kuthengo.+ Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Sungakhale woyera.+ Kodi udzakhalabe wosayera kufikira liti?”+ Zefaniya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsoka kwa iye amene akuchita zinthu zopanduka, amene akudziipitsa, mzinda wopondereza anthu ake.+
27 Chigololo chako,+ kumemesa* kwako,+ khalidwe lako lotayirira la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona zinthu zako zonyansa pamapiri kuthengo.+ Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Sungakhale woyera.+ Kodi udzakhalabe wosayera kufikira liti?”+