Deuteronomo 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anawazula m’dziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu n’kuwataya m’dziko lina monga mmene zilili lero.’+
28 Choncho Yehova anawazula m’dziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu n’kuwataya m’dziko lina monga mmene zilili lero.’+