Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Samala kuti phazi lako lisakhale lopanda nsapato, ndi kuti usachite ludzu.+ Koma iwe unati, ‘Zimenezo ayi!+ Ine ndakondana ndi alendo+ ndipo ndidzawatsatira.’+

  • Yeremiya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pali mawu akuti: “Mwamuna akathetsa ukwati ndi mkazi wake, ndipo mkaziyo n’kuchokadi ndi kukakwatiwa ndi mwamuna wina, sangabwererenso kwa mwamuna woyamba uja.”+

      Kodi dzikoli silinaipitsidwe kale?+

      Yehova wanena kuti: “Iwe wachita uhule ndi amuna ambirimbiri.+ Kodi m’poyenera kuti ubwererenso kwa ine?+

  • Yeremiya 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 ‘Ndithudi, monga mmene mkazi amasiyira mwamuna wake+ mwachinyengo, inunso a m’nyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ watero Yehova.”

  • Hoseya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova anandiuza kuti: “Yambanso kukonda mkazi wokondedwa ndi mwamuna,+ mkazi amene akuchita chigololo. Ukamukonde ngati mmene Yehova akukondera ana a Isiraeli,+ ngakhale kuti iwo akutembenukira kwa milungu ina,+ imene amakonda kuipatsa nsembe za mphesa zouma zoumba pamodzi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena