Yesaya 57:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe unatsetserekera kwa Meleki utatenga mafuta, ndipo unachulukitsa mafuta ako onunkhira.+ Unapitiriza kutumiza nthumwi zako kutali kwambiri moti mpaka unatsitsira zochita zako m’Manda.+ Hoseya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo apita kudziko la Asuri+ ngati mbidzi yoyenda yokha.+ Koma Efuraimu walipira akazi kuti azigona nawo.+
9 Iwe unatsetserekera kwa Meleki utatenga mafuta, ndipo unachulukitsa mafuta ako onunkhira.+ Unapitiriza kutumiza nthumwi zako kutali kwambiri moti mpaka unatsitsira zochita zako m’Manda.+
9 Iwo apita kudziko la Asuri+ ngati mbidzi yoyenda yokha.+ Koma Efuraimu walipira akazi kuti azigona nawo.+