1 Samueli 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwambi wa anthu akale umati, ‘Choipa chimachokera kwa munthu woipa,’+ koma dzanja langali silidzakukhudzani. Ezekieli 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+
13 Mwambi wa anthu akale umati, ‘Choipa chimachokera kwa munthu woipa,’+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.
2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+