Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ahabu anachita zinthu zonyansa kwambiri mwa kutsatira mafano onyansa+ monga momwe Aamori, amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli, anachitira.’”+

  • 2 Mafumu 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma sanamvere,+ ndipo Manase anapitiriza kunyengerera anthu kuti achite zinthu zoipa+ kuposa zimene inkachita mitundu+ yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa ana a Isiraeli.

  • Ezara 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Zinthu zimenezi zitangotha, akalonga+ anabwera kwa ine n’kundiuza kuti: “Aisiraeli, ansembe ndiponso Alevi sanadzipatule+ kwa anthu a mitundu ina pa nkhani ya zinthu zonyansa+ za anthu a mitundu inawo. Anthu ake ndi Akanani,+ Ahiti,+ Aperezi,+ Ayebusi,+ Aamoni,+ Amowabu,+ Aiguputo+ ndi Aamori.+

  • Salimo 106:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iwo anayamba kusakanikirana ndi mitundu ina,+

      Ndi kuyamba kuphunzira zochita zawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena