Mateyu 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndithu ndikukuuzani, Chilango cha Sodomu+ ndi Gomora pa Tsiku la Chiweruzo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha mzinda umenewo.+ Mateyu 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma tsopano ndikukuuzani anthu inu kuti, Chilango cha Sodomu pa Tsiku la Chiweruzo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha Kaperenao.”+
15 Ndithu ndikukuuzani, Chilango cha Sodomu+ ndi Gomora pa Tsiku la Chiweruzo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha mzinda umenewo.+
24 Koma tsopano ndikukuuzani anthu inu kuti, Chilango cha Sodomu pa Tsiku la Chiweruzo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha Kaperenao.”+