Ezekieli 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ngati amazunza munthu wosautsika ndi wosauka,+ ngati amalanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati sabweza chikole,+ ngati amakweza maso ake kuyang’ana mafano onyansa,+ ndiye kuti wachita chinthu chonyansa.+
12 ngati amazunza munthu wosautsika ndi wosauka,+ ngati amalanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati sabweza chikole,+ ngati amakweza maso ake kuyang’ana mafano onyansa,+ ndiye kuti wachita chinthu chonyansa.+