Genesis 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma anthu a ku Sodomu anali oipa, ndipo anali ochimwa kwambiri pamaso pa Yehova.+ Genesis 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anati: “Kudandaula kokhumudwa chifukwa cha Sodomu ndi Gomora+ kwamveka kwambiri, ndipo tchimo lawo n’lalikulu kwambiri.+ Genesis 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anali kufuula kwa Loti kuti: “Kodi amuna amene abwera usiku uno aja, ali kuti? Atulutse kuti tigone nawo.”+
20 Chotero Yehova anati: “Kudandaula kokhumudwa chifukwa cha Sodomu ndi Gomora+ kwamveka kwambiri, ndipo tchimo lawo n’lalikulu kwambiri.+
5 Iwo anali kufuula kwa Loti kuti: “Kodi amuna amene abwera usiku uno aja, ali kuti? Atulutse kuti tigone nawo.”+