Levitiko 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo. Salimo 106:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+
42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.
45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+