Hoseya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzalonjeza kukukwatira kuti ukhale wanga mpaka kalekale.*+ Ndidzalonjeza kukukwatira motsatira chilungamo, komanso chifukwa cha kukoma mtima kwanga kosatha ndi chifundo changa.+
19 Ndidzalonjeza kukukwatira kuti ukhale wanga mpaka kalekale.*+ Ndidzalonjeza kukukwatira motsatira chilungamo, komanso chifukwa cha kukoma mtima kwanga kosatha ndi chifundo changa.+