Ezekieli 20:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ine ndinanena kuti: “Kalanga ine, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Iwo akundinena kuti, ‘Kodi si miyambi imene akunenayi?’”+ Hoseya 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinalankhula ndi aneneri+ ndipo ndinawaonetsa masomphenya ochuluka. Kudzera mwa aneneri, ndinali kupereka mafanizo ambiri.+ Mateyu 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 N’chifukwa chake ndikulankhula nawo mwa mafanizo. Pakuti ngakhale akuona, kuona kwawo n’kopanda phindu. Ngakhale akumva, kumva kwawo n’kopanda phindu, ndipo sazindikira tanthauzo lake.+
49 Ine ndinanena kuti: “Kalanga ine, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Iwo akundinena kuti, ‘Kodi si miyambi imene akunenayi?’”+
10 Ndinalankhula ndi aneneri+ ndipo ndinawaonetsa masomphenya ochuluka. Kudzera mwa aneneri, ndinali kupereka mafanizo ambiri.+
13 N’chifukwa chake ndikulankhula nawo mwa mafanizo. Pakuti ngakhale akuona, kuona kwawo n’kopanda phindu. Ngakhale akumva, kumva kwawo n’kopanda phindu, ndipo sazindikira tanthauzo lake.+