2 Mafumu 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+ 2 Mbiri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.
20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+
13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.