Yesaya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+ Ezekieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+ Ezekieli 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndachititsa chipumi chako kukhala ngati mwala wa dayamondi, cholimba kuposa mwala wa nsangalabwi.+ Usawaope,+ ndipo usachite mantha ndi nkhope zawo,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.”+ Ezekieli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Iwe mwana wa munthu, kodi anthu opanduka a nyumba ya Isiraeli+ sanakufunse kuti, ‘Kodi ukuchita chiyani?’
2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+
5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+
9 Ndachititsa chipumi chako kukhala ngati mwala wa dayamondi, cholimba kuposa mwala wa nsangalabwi.+ Usawaope,+ ndipo usachite mantha ndi nkhope zawo,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.”+
9 “Iwe mwana wa munthu, kodi anthu opanduka a nyumba ya Isiraeli+ sanakufunse kuti, ‘Kodi ukuchita chiyani?’