Deuteronomo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Usagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wako mosasamala,+ pakuti Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake mosasamala osam’langa.+ Yeremiya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngakhale atalumbira kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo!” adzakhala akulumbira mwachinyengo.+
11 “‘Usagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wako mosasamala,+ pakuti Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake mosasamala osam’langa.+