Yesaya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+ Yeremiya 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Meta tsitsi lako lalitalilo ndi kulitaya.+ Ukwere pamapiri opanda mitengo ndi kuimba nyimbo yoimba polira pamenepo,+ pakuti Yehova wakana+ ndi kusiya mbadwo wa anthu amene wawakwiyira.+ Ezekieli 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira+ yokhudza atsogoleri a Isiraeli.+
11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+
29 “Meta tsitsi lako lalitalilo ndi kulitaya.+ Ukwere pamapiri opanda mitengo ndi kuimba nyimbo yoimba polira pamenepo,+ pakuti Yehova wakana+ ndi kusiya mbadwo wa anthu amene wawakwiyira.+