Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Munthu akatemberera bambo ndi mayi ake,+ aziphedwa ndithu.+ Iye watemberera bambo ndi mayi ake. Mlandu wa magazi ake ukhale wa iye mwini.+

  • Levitiko 20:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+

  • Ezekieli 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndikauza munthu woipa kuti, ‘Udzafa ndithu,’+ iwe osamulankhula munthu woipayo ndi kumuchenjeza kuti asiye njira yake yoipa n’cholinga choti akhalebe ndi moyo,+ iyeyo poti ndi woipa adzafa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma magazi ake ndidzawafuna kuchokera m’manja mwako.+

  • Ezekieli 33:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 munthu akamva kulira kwa lipengalo koma osachitapo kanthu,+ lupanga n’kubwera ndi kumupha, magazi ake adzakhala pamutu pake.+

  • Machitidwe 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena