Salimo 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuti pasapezeke wondikhadzulakhadzula ngati mmene mkango umachitira,+Pasapezeke wondikwatula popanda wondilanditsa.+ Nahumu 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi malo obisalamo mikango, phanga la mikango yamphamvu, malo amene mkango unali kuyenda ndi kulowa,+ malo amene munali mwana wa mkango, mmene mikango inali kukhala popanda woiwopsa, ali kuti?+ Zefaniya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga ake anali mikango imene inali kubangula.+ Oweruza ake anali mimbulu yoyenda usiku imene sinatafune mafupa mpaka m’mawa.+
2 Kuti pasapezeke wondikhadzulakhadzula ngati mmene mkango umachitira,+Pasapezeke wondikwatula popanda wondilanditsa.+
11 Kodi malo obisalamo mikango, phanga la mikango yamphamvu, malo amene mkango unali kuyenda ndi kulowa,+ malo amene munali mwana wa mkango, mmene mikango inali kukhala popanda woiwopsa, ali kuti?+
3 Akalonga ake anali mikango imene inali kubangula.+ Oweruza ake anali mimbulu yoyenda usiku imene sinatafune mafupa mpaka m’mawa.+