2 Mafumu 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehoahazi anali ndi zaka 23+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya. 2 Mbiri 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako anthu a m’dzikolo anatenga Yehoahazi+ mwana wa Yosiya n’kumulonga ufumu ku Yerusalemu m’malo mwa bambo ake.+
31 Yehoahazi anali ndi zaka 23+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya.
36 Kenako anthu a m’dzikolo anatenga Yehoahazi+ mwana wa Yosiya n’kumulonga ufumu ku Yerusalemu m’malo mwa bambo ake.+