2 Mbiri 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehoyakimu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+ Yeremiya 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Ndithudi, maso ako ndi mtima wako sizikulakalaka china chilichonse koma phindu lachinyengo,+ anthu osalakwa kuti ukhetse magazi awo+ komanso kuba mwachinyengo ndi kulanda.’
5 Yehoyakimu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+
17 ‘Ndithudi, maso ako ndi mtima wako sizikulakalaka china chilichonse koma phindu lachinyengo,+ anthu osalakwa kuti ukhetse magazi awo+ komanso kuba mwachinyengo ndi kulanda.’