Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo. Ezara 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Panali mafumu amphamvu+ olamulira Yerusalemu ndi dera lonse la kutsidya lina la Mtsinje+ ndipo anali kupatsidwa msonkho umene munthu aliyense amapereka, msonkho wakatundu, ndi msonkho wapanjira.+
17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.
20 Panali mafumu amphamvu+ olamulira Yerusalemu ndi dera lonse la kutsidya lina la Mtsinje+ ndipo anali kupatsidwa msonkho umene munthu aliyense amapereka, msonkho wakatundu, ndi msonkho wapanjira.+