Yesaya 56:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Alendo amene adziphatika kwa Yehova kuti am’tumikire+ ndiponso amene amakonda dzina la Yehova+ n’cholinga choti akhale atumiki ake, onse amene amasunga sabata kuti asalidetse ndiponso amene amatsatira pangano langa,+
6 “Alendo amene adziphatika kwa Yehova kuti am’tumikire+ ndiponso amene amakonda dzina la Yehova+ n’cholinga choti akhale atumiki ake, onse amene amasunga sabata kuti asalidetse ndiponso amene amatsatira pangano langa,+