Levitiko 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chake ndinakuuzani+ kuti: “Inuyo mudzatenga dzikolo ndipo ine ndidzalipereka m’manja mwanu kuti likhale lanu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndakupatulani kwa anthu a mitundu ina.”+ Numeri 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anauza Mose kuti: “Tinakalowa m’dziko limene munatitumako. Ndithudi ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo zipatso zake ndi izi.+
24 N’chifukwa chake ndinakuuzani+ kuti: “Inuyo mudzatenga dzikolo ndipo ine ndidzalipereka m’manja mwanu kuti likhale lanu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndakupatulani kwa anthu a mitundu ina.”+
27 Anauza Mose kuti: “Tinakalowa m’dziko limene munatitumako. Ndithudi ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo zipatso zake ndi izi.+