Deuteronomo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ Salimo 81:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+
10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+