Genesis 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anati: “Tiyeni timange mzinda wathuwathu, ndipo nsanja yake ikafike m’mwamba mwenimweni.+ Tikatero tidzipangira dzina loti titchuke nalo,+ ndipo sitibalalikana padziko lonse lapansi.”+ Mateyu 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwenso Kaperenao,+ kodi udzakwezedwa kumwamba kapena? Ku Manda*+ n’kumene udzatsikira ndithu,+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Sodomu, mzindawo ukanakhala ulipobe mpaka lero.
4 Ndiyeno anati: “Tiyeni timange mzinda wathuwathu, ndipo nsanja yake ikafike m’mwamba mwenimweni.+ Tikatero tidzipangira dzina loti titchuke nalo,+ ndipo sitibalalikana padziko lonse lapansi.”+
23 Iwenso Kaperenao,+ kodi udzakwezedwa kumwamba kapena? Ku Manda*+ n’kumene udzatsikira ndithu,+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Sodomu, mzindawo ukanakhala ulipobe mpaka lero.