Danieli 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Nditagona pabedi langa, ndinapitiriza kuona masomphenya ndipo ndinangoona mlonda+ woyera+ akutsika kuchokera kumwamba.
13 “‘Nditagona pabedi langa, ndinapitiriza kuona masomphenya ndipo ndinangoona mlonda+ woyera+ akutsika kuchokera kumwamba.