Danieli 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mtima wake usinthidwe kuchoka kumtima wa munthu n’kukhala mtima wa nyama+ ndipo padutse nthawi zokwanira 7.+ Luka 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.
16 Mtima wake usinthidwe kuchoka kumtima wa munthu n’kukhala mtima wa nyama+ ndipo padutse nthawi zokwanira 7.+
24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.