Danieli 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Chonde, yesani atumiki anufe kwa masiku 10. Lolani kuti azitipatsa zakudya zamasamba+ ndi madzi oti tizimwa.
12 “Chonde, yesani atumiki anufe kwa masiku 10. Lolani kuti azitipatsa zakudya zamasamba+ ndi madzi oti tizimwa.