2 Mbiri 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+ Danieli 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Popeza ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndiye akulamulira kumwamba.+
13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+
26 “‘Popeza ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndiye akulamulira kumwamba.+