Genesis 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe wotimasulira malotowo.” Pamenepo Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu sindiye amamasulira?+ Tandifotokozerani malotowo.” Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:
8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe wotimasulira malotowo.” Pamenepo Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu sindiye amamasulira?+ Tandifotokozerani malotowo.”
28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: