Danieli 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+ Danieli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’chaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero,+ wa mtundu wa Amedi,+ amene anaikidwa kukhala mfumu ya ufumu wa Akasidi,+
6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+
9 M’chaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero,+ wa mtundu wa Amedi,+ amene anaikidwa kukhala mfumu ya ufumu wa Akasidi,+