Salimo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzatamanda Yehova nthawi zonse.+Ndidzamutamanda ndi pakamwa panga mosalekeza.+ Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani ndi chiyembekezocho.+ Pirirani chisautso.+ Limbikirani kupemphera.+